2 Samueli 22:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mudzachititsa kuti adani anga athawe pamaso panga;+Ndidzapha* anthu amene amadana nane.+