2 Samueli 22:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Inu mudzandipulumutsa kwa anthu a mtundu wanga ondipezera zifukwa.+ Mudzanditeteza kuti ndikhale mtsogoleri wa mitundu ya anthu.+Anthu amene sindikuwadziwa adzanditumikira.+
44 Inu mudzandipulumutsa kwa anthu a mtundu wanga ondipezera zifukwa.+ Mudzanditeteza kuti ndikhale mtsogoleri wa mitundu ya anthu.+Anthu amene sindikuwadziwa adzanditumikira.+