2 Samueli 22:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Iye amachita zazikulu kuti apulumutse mfumu yake;+Amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa wodzozedwa wake,Kwa Davide ndi mbadwa* zake mpaka kalekale.”+
51 Iye amachita zazikulu kuti apulumutse mfumu yake;+Amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa wodzozedwa wake,Kwa Davide ndi mbadwa* zake mpaka kalekale.”+