-
2 Samueli 23:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Benaya anaphanso munthu wamkulu modabwitsa wa ku Iguputo. Ngakhale kuti munthuyu anali ndi mkondo mʼmanja mwake, Benaya anapita kukakumana naye atanyamula ndodo, ndipo analanda mkondowo nʼkumupha ndi mkondo wake womwewo.
-