2 Samueli 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anawoloka Yorodano nʼkukamanga msasa ku Aroweli,+ kumanja* kwa mzinda umene unali pakati pa chigwa.* Atatero anapita kufupi ndi dera la fuko la Gadi ndipo kenako anapita ku Yazeri.+
5 Anawoloka Yorodano nʼkukamanga msasa ku Aroweli,+ kumanja* kwa mzinda umene unali pakati pa chigwa.* Atatero anapita kufupi ndi dera la fuko la Gadi ndipo kenako anapita ku Yazeri.+