2 Samueli 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atachoka kumeneko anafika ku Giliyadi+ ndi ku Tatimu-hodisi, ndipo anapitirira mpaka ku Dani-jaana nʼkuzungulira kukafika ku Sidoni.+
6 Atachoka kumeneko anafika ku Giliyadi+ ndi ku Tatimu-hodisi, ndipo anapitirira mpaka ku Dani-jaana nʼkuzungulira kukafika ku Sidoni.+