-
1 Mafumu 1:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Choncho atumiki ake anamuuza kuti: “Mbuyathu mfumu, bwanji tikufunireni mtsikana yemwe ndi namwali woti azikusamalirani? Azigona pafupi nanu kuti inu mbuyathu mfumu muzimva kutentha.”
-