1 Mafumu 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma bambo ake sanamʼdzudzulepo* nʼkumufunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani ukuchita zimenezi?” Iye analinso wooneka bwino kwambiri ndipo mayi ake anamʼbereka Abisalomu atabadwa kale.
6 Koma bambo ake sanamʼdzudzulepo* nʼkumufunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani ukuchita zimenezi?” Iye analinso wooneka bwino kwambiri ndipo mayi ake anamʼbereka Abisalomu atabadwa kale.