1 Mafumu 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zitatero, Bati-seba anapita kuchipinda kumene kunali mfumu. Mfumuyo inali yokalamba kwambiri ndipo Abisagi+ wa ku Sunemu ankaisamalira.
15 Zitatero, Bati-seba anapita kuchipinda kumene kunali mfumu. Mfumuyo inali yokalamba kwambiri ndipo Abisagi+ wa ku Sunemu ankaisamalira.