1 Mafumu 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Bati-seba anayankha kuti: “Mbuyanga, ndinu amene munalumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wanu kwa ine kapolo wanu kuti, ‘Mwana wako Solomo ndi amene adzakhale mfumu pambuyo panga ndipo iye ndi amene adzakhale pampando wanga wachifumu.’+
17 Bati-seba anayankha kuti: “Mbuyanga, ndinu amene munalumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wanu kwa ine kapolo wanu kuti, ‘Mwana wako Solomo ndi amene adzakhale mfumu pambuyo panga ndipo iye ndi amene adzakhale pampando wanga wachifumu.’+