-
1 Mafumu 1:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Nthawi yomweyo anthu anauza mfumu kuti: “Kwabwera mneneri Natani!” Kenako Natani anagwada nʼkuweramira mfumuyo mpaka nkhope yake kufika pansi.
-