1 Mafumu 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Natani anati: “Mbuyanga mfumu, kodi munanena kuti, ‘Adoniya adzakhala mfumu pambuyo panga ndipo ndi amene adzakhale pampando wanga wachifumuʼ?+
24 Ndiyeno Natani anati: “Mbuyanga mfumu, kodi munanena kuti, ‘Adoniya adzakhala mfumu pambuyo panga ndipo ndi amene adzakhale pampando wanga wachifumuʼ?+