-
1 Mafumu 1:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 zimene ndinakulumbirira mʼdzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli kuti, ‘Mwana wako Solomo adzakhala mfumu pambuyo panga ndipo iye ndi amene adzakhale pampando wanga wachifumu mʼmalo mwanga,’ ndi zimene ndichite lero.”
-