1 Mafumu 1:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nthawi yomweyo Mfumu Davide inati: “Ndiitanireni wansembe Zadoki, mneneri Natani ndi Benaya+ mwana wa Yehoyada.”+ Ndipo anthuwo anabweradi.
32 Nthawi yomweyo Mfumu Davide inati: “Ndiitanireni wansembe Zadoki, mneneri Natani ndi Benaya+ mwana wa Yehoyada.”+ Ndipo anthuwo anabweradi.