-
1 Mafumu 1:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Ndiye pobwera muzikamulondola, ndipo adzafike kuno nʼkukhala pampando wanga wachifumu. Iyeyo adzakhala mfumu mʼmalo mwanga ndipo ndidzamuika kukhala mtsogoleri wa Isiraeli ndi Yuda.”
-