1 Mafumu 1:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Nthawi yomweyo Benaya mwana wa Yehoyada anayankha mfumu kuti: “Ame!* Yehova, Mulungu wa mbuyanga mfumu, atsimikizire zimenezi.
36 Nthawi yomweyo Benaya mwana wa Yehoyada anayankha mfumu kuti: “Ame!* Yehova, Mulungu wa mbuyanga mfumu, atsimikizire zimenezi.