1 Mafumu 1:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Adoniya ndi anthu onse amene anawaitana anamva phokosolo, ndipo anali atangomaliza kudya.+ Yowabu atangomva kulira kwa lipenga anafunsa kuti: “Kodi phokoso likumveka mumzindali ndi la chiyani?”
41 Adoniya ndi anthu onse amene anawaitana anamva phokosolo, ndipo anali atangomaliza kudya.+ Yowabu atangomva kulira kwa lipenga anafunsa kuti: “Kodi phokoso likumveka mumzindali ndi la chiyani?”