-
1 Mafumu 1:49Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
49 Anthu onse amene anaitanidwa ndi Adoniya anachita mantha ndipo ananyamuka nʼkumapita.