-
1 Mafumu 1:51Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
51 Solomo anauzidwa kuti: “Adoniya akuchita mantha ndi inu Mfumu Solomo moti wakagwira nyanga za guwa lansembe, ndipo wanena kuti, ‘Mfumu Solomo andilumbirire kaye ine mtumiki wake kuti sandipha ndi lupanga.’”
-