-
1 Mafumu 1:53Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
53 Choncho Mfumu Solomo inatumiza anthu kuti akatenge Adoniya paguwa lansembe nʼkubwera naye. Kenako Adoniya analowa nʼkugwadira Mfumu Solomo. Ndiyeno Solomo anamuuza kuti: “Pita kunyumba kwako.”
-