1 Mafumu 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Adoniya anapitiriza kuti: “Inu mukudziwa kuti ufumu unayenera kukhala wanga, ndipo Aisiraeli onse ankayembekezera kuti ineyo ndikhala mfumu.+ Koma ufumuwo unatembenuka nʼkukhala wa mchimwene wanga, chifukwa Yehova ndi amene anamupatsa ufumuwo.+
15 Adoniya anapitiriza kuti: “Inu mukudziwa kuti ufumu unayenera kukhala wanga, ndipo Aisiraeli onse ankayembekezera kuti ineyo ndikhala mfumu.+ Koma ufumuwo unatembenuka nʼkukhala wa mchimwene wanga, chifukwa Yehova ndi amene anamupatsa ufumuwo.+