-
1 Mafumu 2:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Choncho Bati-seba anapita kwa Mfumu Solomo kukafotokoza zomwe Adoniya anamutuma. Atangofika, Solomo anaimirira kuti akumane naye ndipo anamuweramira. Kenako anakhala pampando wake wachifumu nʼkuitanitsa mpando wina ndipo anauika kumanja kwake kuti amayi akewo akhalepo.
-