-
1 Mafumu 2:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Choncho Bati-seba anapitiriza kuti: “Ndimapempha kuti Abisagi wa ku Sunemu mumupereke kwa mchimwene wanu Adoniya kuti akhale mkazi wake.”
-