-
1 Mafumu 2:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Benaya anapitadi kuchihema cha Yehova nʼkukamuuza Yowabu kuti: “Mfumu ikuti utuluke.” Koma iye anati: “Ayi! Ndifera momʼmuno.” Ndiyeno Benaya anakauza mfumu kuti: “Yowabu wanena zimenezi, ndipo wandiyankha choncho.”
-