1 Mafumu 2:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Magazi awo adzakhala pamutu pa Yowabu ndi pamutu pa mbadwa zake mpaka kalekale.+ Koma mtendere wochokera kwa Yehova ukhale kwa Davide, mbadwa zake, nyumba yake ndiponso mpando wake wachifumu mpaka kalekale.”
33 Magazi awo adzakhala pamutu pa Yowabu ndi pamutu pa mbadwa zake mpaka kalekale.+ Koma mtendere wochokera kwa Yehova ukhale kwa Davide, mbadwa zake, nyumba yake ndiponso mpando wake wachifumu mpaka kalekale.”