1 Mafumu 2:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zitatero, mfumu inasankha Benaya+ mwana wa Yehoyada kuti akhale mkulu wa asilikali mʼmalo mwa Yowabu, ndipo inasankha wansembe Zadoki+ kuti alowe mʼmalo mwa Abiyatara.
35 Zitatero, mfumu inasankha Benaya+ mwana wa Yehoyada kuti akhale mkulu wa asilikali mʼmalo mwa Yowabu, ndipo inasankha wansembe Zadoki+ kuti alowe mʼmalo mwa Abiyatara.