-
1 Mafumu 2:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Simeyi anayankha mfumu kuti: “Mwanena bwino. Ine mtumiki wanu ndichita zimene mbuyanga mfumu mwanena.” Ndipo Simeyi anakhala ku Yerusalemu masiku ambiri.
-