-
1 Mafumu 2:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Nthawi yomweyo, Simeyi anakwera bulu wake nʼkupita ku Gati kwa Akisi kukafunafuna akapolo akewo. Simeyi atabwerako ku Gati ndi akapolo akewo,
-