1 Mafumu 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Solomo anapitiriza kukonda Yehova ndipo ankatsatira malamulo a Davide bambo ake, kungoti ankapereka nsembe zopsereza pamalo okwezeka.+
3 Solomo anapitiriza kukonda Yehova ndipo ankatsatira malamulo a Davide bambo ake, kungoti ankapereka nsembe zopsereza pamalo okwezeka.+