1 Mafumu 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Solomo atadzuka, anazindikira kuti waona masomphenya. Kenako anapita ku Yerusalemu nʼkukaima patsogolo pa likasa la pangano la Yehova. Ndiyeno anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano+ ndipo anakonzera phwando atumiki ake onse.
15 Solomo atadzuka, anazindikira kuti waona masomphenya. Kenako anapita ku Yerusalemu nʼkukaima patsogolo pa likasa la pangano la Yehova. Ndiyeno anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano+ ndipo anakonzera phwando atumiki ake onse.