-
1 Mafumu 3:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Patapita masiku atatu kuchokera tsiku limene ine ndinabereka mwana, nayenso anabereka mwana wamwamuna. Tinali awiriwiri mʼnyumbamo ndipo munalibe munthu wina aliyense.
-