-
1 Mafumu 3:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ndiyeno ine kapolo wanu ndili mʼtulo, mayiyu anadzuka pakati pa usiku nʼkutenga mwana wanga amene anali pambali panga nʼkumuika pachifuwa pake. Ndipo anatenga mwana wake wakufayo nʼkumuika pachifuwa panga.
-