-
1 Mafumu 3:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Nditadzuka kuti ndiyamwitse mwana wanga, ndinapeza kuti anali wakufa. Choncho ndinamuyangʼanitsitsa mʼmawa nʼkuona kuti si mwana wanga amene ndinabereka.”
-