-
1 Mafumu 3:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Koma mayi winayo anati: “Ayi, mwana wanga ndi wamoyoyu, wako ndi wakufayo!” Ndipo mayi woyamba uja ankanena kuti: “Ayi, mwana wako ndi wakufayu, wanga ndi wamoyoyo.” Iwo anapitiriza kukangana chonchi pamaso pa mfumu.
-