1 Mafumu 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Geberi mwana wa Uri ankayangʼanira ku Giliyadi,+ mʼdera la Sihoni+ mfumu ya Aamori ndi la Ogi+ mfumu ya Basana. Panalinso nduna imodzi yomwe inkayangʼanira nduna zonsezi mʼdzikomo.
19 Geberi mwana wa Uri ankayangʼanira ku Giliyadi,+ mʼdera la Sihoni+ mfumu ya Aamori ndi la Ogi+ mfumu ya Basana. Panalinso nduna imodzi yomwe inkayangʼanira nduna zonsezi mʼdzikomo.