1 Mafumu 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Nduna zinkapititsa chakudya cha Mfumu Solomo komanso anthu onse amene ankadya ndi mfumuyo. Nduna iliyonse inkapereka chakudya cha mwezi umodzi ndipo inkaonetsetsa kuti ndi chokwanira bwino.+
27 Nduna zinkapititsa chakudya cha Mfumu Solomo komanso anthu onse amene ankadya ndi mfumuyo. Nduna iliyonse inkapereka chakudya cha mwezi umodzi ndipo inkaonetsetsa kuti ndi chokwanira bwino.+