-
1 Mafumu 4:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Ndunazi zinkabweretsanso balere ndi chakudya cha mahatchi okoka magaleta ndiponso cha mahatchi ena. Zinkachipititsa kulikonse komwe chikufunika, aliyense mogwirizana ndi zomwe walamulidwa.
-