1 Mafumu 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anamanga zipinda zamʼmbali zosanjikizana kuzungulira nyumbayo+ ndipo chipinda chilichonse chinali chachitali mikono 5. Zipindazo anazilumikiza kunyumbayo ndi matabwa a mkungudza.
10 Anamanga zipinda zamʼmbali zosanjikizana kuzungulira nyumbayo+ ndipo chipinda chilichonse chinali chachitali mikono 5. Zipindazo anazilumikiza kunyumbayo ndi matabwa a mkungudza.