1 Mafumu 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye anakonza chipinda chamkati+ cha nyumbayo kuti aikemo likasa la pangano la Yehova.+