-
1 Mafumu 6:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Phiko limodzi la kerubi linali lalitali mikono 5 ndipo phiko lina, linalinso lalitali mikono 5. Kuchokera kunsonga kwa phiko kukafika kunsonga kwa phiko lina kutalika kwake kunali mikono 10.
-