1 Mafumu 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ansembe anabweretsa likasa la pangano la Yehova pamalo ake,+ kuchipinda chamkati cha nyumbayo, chomwe ndi Malo Oyera Koposa, ndipo analiika pansi pa mapiko a akerubi.+
6 Kenako ansembe anabweretsa likasa la pangano la Yehova pamalo ake,+ kuchipinda chamkati cha nyumbayo, chomwe ndi Malo Oyera Koposa, ndipo analiika pansi pa mapiko a akerubi.+