-
1 Mafumu 8:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma Yehova anauza Davide bambo anga kuti, ‘Unkafunitsitsa kumanga nyumba ya dzina langa ndipo unachita bwino kulakalaka utachita zimenezi.
-