1 Mafumu 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Kumwamba, ngakhalenso kumwamba kwa kumwamba, simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba imene ndamangayi?+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:27 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,
27 Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Kumwamba, ngakhalenso kumwamba kwa kumwamba, simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba imene ndamangayi?+