1 Mafumu 8:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 ndiyeno munthu aliyense kapena anthu anu onse Aisiraeli akapereka pemphero lililonse, akapempha kuti muwachitire chifundo+ (chifukwa aliyense akudziwa ululu umene uli mumtima mwake),+ ndiponso akakweza manja awo atayangʼana kunyumbayi,
38 ndiyeno munthu aliyense kapena anthu anu onse Aisiraeli akapereka pemphero lililonse, akapempha kuti muwachitire chifundo+ (chifukwa aliyense akudziwa ululu umene uli mumtima mwake),+ ndiponso akakweza manja awo atayangʼana kunyumbayi,