1 Mafumu 8:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 inuyo mumve muli kumwambako, komwe mumakhala+ ndipo mukhululuke+ ndi kuchitapo kanthu. Mupereke mphoto kwa aliyense mogwirizana ndi njira zake zonse,+ chifukwa mukudziwa mtima wake (inu nokha mumadziwa bwino mtima wa munthu aliyense).+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:39 Galamukani!,4/2011, tsa. 28
39 inuyo mumve muli kumwambako, komwe mumakhala+ ndipo mukhululuke+ ndi kuchitapo kanthu. Mupereke mphoto kwa aliyense mogwirizana ndi njira zake zonse,+ chifukwa mukudziwa mtima wake (inu nokha mumadziwa bwino mtima wa munthu aliyense).+