1 Mafumu 8:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Anthu anu akapita kunkhondo kukamenyana ndi adani awo mmene mwawatumizira,+ ndipo akapemphera+ kwa Yehova atayangʼana kumzinda umene mwasankha+ ndi kunyumba ya dzina lanu imene ndamanga,+
44 Anthu anu akapita kunkhondo kukamenyana ndi adani awo mmene mwawatumizira,+ ndipo akapemphera+ kwa Yehova atayangʼana kumzinda umene mwasankha+ ndi kunyumba ya dzina lanu imene ndamanga,+