1 Mafumu 8:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Makutu anu amve pempho* la mtumiki wanu lopempha chifundo+ komanso pempho la anthu anu Aisiraeli lopempha chifundo, powamvera zonse zimene angakupempheni.+
52 Makutu anu amve pempho* la mtumiki wanu lopempha chifundo+ komanso pempho la anthu anu Aisiraeli lopempha chifundo, powamvera zonse zimene angakupempheni.+