1 Mafumu 8:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Chifukwa munawasankha pakati pa mitundu yonse ya anthu apadziko lapansi+ kuti akhale cholowa chanu ngati mmene munanenera kudzera mwa Mose mtumiki wanu, pamene munkatulutsa makolo athu mu Iguputo, inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.”
53 Chifukwa munawasankha pakati pa mitundu yonse ya anthu apadziko lapansi+ kuti akhale cholowa chanu ngati mmene munanenera kudzera mwa Mose mtumiki wanu, pamene munkatulutsa makolo athu mu Iguputo, inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.”