-
1 Mafumu 8:59Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
59 Mawu amene ndanenawa popempha chifundo kwa Yehova, Yehova Mulungu wathu aziwakumbukira masana komanso usiku, kuti aonetsetse kuti chilungamo chachitika kwa mtumiki wake ndiponso kwa anthu ake Aisiraeli, mogwirizana ndi zimene zingafunike tsiku lililonse.
-