1 Mafumu 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iweyo ukayenda mʼnjira zanga ngati mmene bambo ako Davide anachitira,+ yemwe anali ndi mtima wokhulupirika+ komanso ankachita zoyenera,+ ukachita zonse zimene ndinakulamula,+ ndiponso ukamamvera malangizo anga ndi ziweruzo zanga,+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:4 Nsanja ya Olonda,11/15/2012, tsa. 78/15/2007, tsa. 125/1/1997, tsa. 5
4 Iweyo ukayenda mʼnjira zanga ngati mmene bambo ako Davide anachitira,+ yemwe anali ndi mtima wokhulupirika+ komanso ankachita zoyenera,+ ukachita zonse zimene ndinakulamula,+ ndiponso ukamamvera malangizo anga ndi ziweruzo zanga,+